Ekisodo 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Matalalawo anawononga dziko lonse la Iguputo. Anawononga china chilichonse, munthu kapena nyama, ndi mitundu yonse ya zomera zam’munda. Anagwetsanso mitundu yonse ya mitengo.+
25 Matalalawo anawononga dziko lonse la Iguputo. Anawononga china chilichonse, munthu kapena nyama, ndi mitundu yonse ya zomera zam’munda. Anagwetsanso mitundu yonse ya mitengo.+