Salimo 106:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo anakhulupirira mawu ake,+Ndipo anayamba kumuimbira nyimbo zomutamanda.+ Yesaya 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unasandutsa pansi pa nyanja kukhala njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+
10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unasandutsa pansi pa nyanja kukhala njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+