Miyambo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Nzeru ndi malangizo zimanyozedwa ndi zitsiru.*+ Maliro 3:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kodi munthu angadandaulirenji+ chifukwa cha zotsatirapo za tchimo lake?+