Salimo 73:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+ Yakobo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwalidyerera dziko lapansi ndipo mwasangalala.+ Mwanenepetsa mitima yanu pa tsiku lokaphedwa.+
12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+