Salimo 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti amene ananditonza si mdani.+Akanakhala mdani ndikanapirira.Amene anadzikweza pamaso panga si munthu wodana nane kwambiri.+Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.+
12 Pakuti amene ananditonza si mdani.+Akanakhala mdani ndikanapirira.Amene anadzikweza pamaso panga si munthu wodana nane kwambiri.+Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.+