2 Mafumu 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano khate+ la Namani limamatira iweyo ndi mbadwa zako mpaka kalekale.”*+ Nthawi yomweyo Gehazi anachoka pamaso pa Elisa, atachita khate loyera kuti mbuu.+
27 Tsopano khate+ la Namani limamatira iweyo ndi mbadwa zako mpaka kalekale.”*+ Nthawi yomweyo Gehazi anachoka pamaso pa Elisa, atachita khate loyera kuti mbuu.+