Salimo 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mulungu woona Ndiye amandilimbitsa,*+Ndipo adzasalaza njira yanga.+ Salimo 118:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ya ndiye malo anga obisalapo ndi mphamvu zanga,+Iye amandipulumutsa.+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
32 Mulungu woona Ndiye amandilimbitsa,*+Ndipo adzasalaza njira yanga.+ Salimo 118:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ya ndiye malo anga obisalapo ndi mphamvu zanga,+Iye amandipulumutsa.+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+