Machitidwe 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Sitefano, anali wodzazidwa ndi chisomo komanso mphamvu, ndipo anali kuchita zodabwitsa ndi zizindikiro zazikulu+ pakati pa anthu.
8 Tsopano Sitefano, anali wodzazidwa ndi chisomo komanso mphamvu, ndipo anali kuchita zodabwitsa ndi zizindikiro zazikulu+ pakati pa anthu.