Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+ Salimo 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Asungunuke ndi kupita ngati madzi.+Mulungu akunge uta woponyera mivi yake pamene adaniwo akugwa.+