Salimo 113:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dzina la Yehova lidalitsike,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+ Danieli 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anati: “Dzina la Mulungu likhale lotamandika+ kuyambira kalekale mpaka kalekale, pakuti nzeru ndi mphamvu ndi zake.+
20 Iye anati: “Dzina la Mulungu likhale lotamandika+ kuyambira kalekale mpaka kalekale, pakuti nzeru ndi mphamvu ndi zake.+