Deuteronomo 1:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Kumeneko Aamori okhala m’phiri limenelo anatuluka kudzakumana nanu ndipo anakuthamangitsani,+ mmene njuchi zimachitira, ndi kukubalalitsani m’phiri la Seiri mpaka kukafika ku Horima.+
44 Kumeneko Aamori okhala m’phiri limenelo anatuluka kudzakumana nanu ndipo anakuthamangitsani,+ mmene njuchi zimachitira, ndi kukubalalitsani m’phiri la Seiri mpaka kukafika ku Horima.+