Salimo 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova, pulumutsani mfumu!+Tsiku limene tidzaitana, Mulungu adzatiyankha.+ 1 Timoteyo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimenezi ndi zabwino ndiponso ndi zovomerezeka+ kwa Mpulumutsi wathu Mulungu,+