Salimo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+ Salimo 44:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti miyoyo yathu yasautsika.+Mimba zathu zili thasa! padothi.
15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+