Salimo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tetezani moyo wanga ndi kundilanditsa.+Musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndathawira kwa inu.+ Salimo 119:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Mtima wanga usunge malangizo anu mosalakwitsa kanthu,+Kuti ndisachite manyazi.+
20 Tetezani moyo wanga ndi kundilanditsa.+Musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndathawira kwa inu.+