Salimo 119:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akalonga asonkhana pamodzi kuti akambirane zondiukira.+Koma ine mtumiki wanu, ndimasinkhasinkha malangizo anu.+ Salimo 119:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Zili bwino kuti ndasautsika,+Kuti ndiphunzire malamulo anu.+
23 Akalonga asonkhana pamodzi kuti akambirane zondiukira.+Koma ine mtumiki wanu, ndimasinkhasinkha malangizo anu.+