Salimo 71:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ine ndidzayembekezera inu nthawi zonse,+Ndipo ndidzakutamandani mowirikiza kuposa kale.