Salimo 106:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo anakhulupirira mawu ake,+Ndipo anayamba kumuimbira nyimbo zomutamanda.+