Genesis 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Potsirizira pake, madzi anamuthera+ m’thumba lachikopa lija, ndipo iye anangomusiya+ mwana uja pachitsamba. Salimo 56:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mwalemba za kuthawathawa kwanga.+Sungani misozi yanga m’thumba lanu lachikopa.+Kodi misozi yanga sili m’buku lanu?+
15 Potsirizira pake, madzi anamuthera+ m’thumba lachikopa lija, ndipo iye anangomusiya+ mwana uja pachitsamba.
8 Inu mwalemba za kuthawathawa kwanga.+Sungani misozi yanga m’thumba lanu lachikopa.+Kodi misozi yanga sili m’buku lanu?+