Salimo 119:90 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+
90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+