Salimo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adzachititsa ofatsa kutsatira zigamulo zake,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuyenda m’njira yake.+ Salimo 119:156 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 156 Chifundo chanu n’chachikulu, inu Yehova.+Ndisungenibe wamoyo mogwirizana ndi zigamulo zanu.+