2 Samueli 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Inu Yehova ndinu nyale yanga,+Ndipo Yehova ndiye amandiunikira pamene ndili mu mdima.+ Salimo 132:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ku Ziyoniko ndidzakulitsa nyanga* ya Davide.+Wodzozedwa wanga ndamukonzera nyale.+