Deuteronomo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu. Salimo 119:75 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 75 Inu Yehova, ndikudziwa bwino kuti zigamulo zanu ndi zolungama,+Ndiponso kuti mwandilanga chifukwa chakuti ndinu wokhulupirika.+
4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu.
75 Inu Yehova, ndikudziwa bwino kuti zigamulo zanu ndi zolungama,+Ndiponso kuti mwandilanga chifukwa chakuti ndinu wokhulupirika.+