2 Mbiri 32:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atumiki a Senakeribuwo analankhula zinthu zinanso zonyoza Yehova Mulungu woona+ ndi Hezekiya mtumiki wake.
16 Atumiki a Senakeribuwo analankhula zinthu zinanso zonyoza Yehova Mulungu woona+ ndi Hezekiya mtumiki wake.