2 Mbiri 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndidzasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko, ndiponso ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+ Salimo 87:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova amakonda kwambiri zipata za Ziyoni+Kusiyana ndi mahema onse a Yakobo.+ Salimo 100:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lowani pazipata zake ndi mawu oyamikira,+Lowani m’mabwalo ake ndi mawu otamanda.+Muyamikeni, tamandani dzina lake.+
6 Koma ndidzasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko, ndiponso ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+
4 Lowani pazipata zake ndi mawu oyamikira,+Lowani m’mabwalo ake ndi mawu otamanda.+Muyamikeni, tamandani dzina lake.+