2 Samueli 22:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye akuphunzitsa manja anga kumenya nkhondo.+Ndipo manja anga akukunga uta wamkuwa.+