Miyambo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chisoti chaulemu cha anthu okalamba ndicho zidzukulu zawo,+ ndipo ana amalemekezeka ndi bambo awo.+ Miyambo 31:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana ake amaimirira n’kumuuza kuti ndi wodala.+ Mwamuna wake amaimirira n’kumutamanda kuti:+
6 Chisoti chaulemu cha anthu okalamba ndicho zidzukulu zawo,+ ndipo ana amalemekezeka ndi bambo awo.+