1 Samueli 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atumiki a Sauli anapita kukauza Davide mawu amenewa, koma Davide anawayankha kuti: “Kodi mukuona ngati ndi nkhani yaing’ono kuchita mgwirizano wa ukwati ndi mfumu, pamene ine ndine munthu wosauka+ ndi wonyozeka?”+ Salimo 138:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti Yehova ali pamwamba, amaona wodzichepetsa,+Koma wodzikuza samuyandikira.+ Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+
23 Atumiki a Sauli anapita kukauza Davide mawu amenewa, koma Davide anawayankha kuti: “Kodi mukuona ngati ndi nkhani yaing’ono kuchita mgwirizano wa ukwati ndi mfumu, pamene ine ndine munthu wosauka+ ndi wonyozeka?”+