1 Mbiri 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mupatse Solomo mwana wanga mtima wathunthu+ kuti asunge malamulo anu,+ maumboni* anu,+ ndi kuti achite zonse. Ndiponso kuti amange chinyumba chachikulu+ chimene ndakonzeratu zipangizo zake.”+ Salimo 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+
19 Mupatse Solomo mwana wanga mtima wathunthu+ kuti asunge malamulo anu,+ maumboni* anu,+ ndi kuti achite zonse. Ndiponso kuti amange chinyumba chachikulu+ chimene ndakonzeratu zipangizo zake.”+
10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+