2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 1 Mbiri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+ Salimo 89:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndidzakhazikitsa mbewu yake kwamuyaya,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhalapo kwa masiku ochuluka ngati masiku a kumwamba.+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
29 Ndidzakhazikitsa mbewu yake kwamuyaya,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhalapo kwa masiku ochuluka ngati masiku a kumwamba.+