Chivumbulutso 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, kunamveka mawu ochokera kumpando wachifumu akuti: “Muzitamanda Mulungu wathu, inu nonse akapolo+ ake, inu omuopa, olemekezeka ndi onyozeka omwe.”+
5 Komanso, kunamveka mawu ochokera kumpando wachifumu akuti: “Muzitamanda Mulungu wathu, inu nonse akapolo+ ake, inu omuopa, olemekezeka ndi onyozeka omwe.”+