2 Samueli 22:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Alendo adzabwera kwa ine akunthunthumira.+Anthu adzamvetsera mawu anga ndi kuwatsatira.+