Ekisodo 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ndiyeno m’tsogolo, mwana wanu akadzakufunsani+ kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ Mudzamuyankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi mphamvu ya dzanja lake mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo.+ Yeremiya 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu munatulutsa anthu anu Aisiraeli m’dziko la Iguputo+ pogwiritsa ntchito zizindikiro, zozizwitsa,+ dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi zinthu zochititsa mantha kwambiri.+
14 “Ndiyeno m’tsogolo, mwana wanu akadzakufunsani+ kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ Mudzamuyankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi mphamvu ya dzanja lake mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo.+
21 Inu munatulutsa anthu anu Aisiraeli m’dziko la Iguputo+ pogwiritsa ntchito zizindikiro, zozizwitsa,+ dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi zinthu zochititsa mantha kwambiri.+