Salimo 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye adzagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuiika pansi pathu.+Adzagonjetsa anthu a mitundu ina ndi kuwaika pansi pa mapazi athu.+ 1 Akorinto 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti ayenera kulamulira monga mfumu kufikira Mulungu ataika adani onse pansi pa mapazi+ ake.
3 Iye adzagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuiika pansi pathu.+Adzagonjetsa anthu a mitundu ina ndi kuwaika pansi pa mapazi athu.+