Yobu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munandiveka khungu ndiponso mnofu,Ndipo munandiluka ndi mafupa ndi mitsempha.+ Mlaliki 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga momwe sudziwira mmene mzimu umagwirira ntchito m’thupi la mwana amene ali m’mimba mwa mayi ake,+ momwemonso sudziwa ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+
5 Monga momwe sudziwira mmene mzimu umagwirira ntchito m’thupi la mwana amene ali m’mimba mwa mayi ake,+ momwemonso sudziwa ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+