Yobu 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi amene anandipanga m’mimba si amene anapanganso iyeyo?+Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe m’mimba?
15 Kodi amene anandipanga m’mimba si amene anapanganso iyeyo?+Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe m’mimba?