Yesaya 64:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ngati momwe zimakhalira moto ukayatsa tchire la zitsamba ndiponso ukawiritsa madzi. Zikanakhala bwino mukanachita zimenezi kuti dzina lanu lidziwike kwa adani anu,+ ndiponso kuti mitundu ya anthu igwedezeke chifukwa cha inu.+
2 ngati momwe zimakhalira moto ukayatsa tchire la zitsamba ndiponso ukawiritsa madzi. Zikanakhala bwino mukanachita zimenezi kuti dzina lanu lidziwike kwa adani anu,+ ndiponso kuti mitundu ya anthu igwedezeke chifukwa cha inu.+