1 Samueli 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi anthu a mumzinda wa Keila adzandipereka m’manja mwake? Kodi Sauli abweradi kuno monga mmene ine mtumiki wanu ndamvera? Yehova Mulungu wa Isiraeli, ndiuzeni ine mtumiki wanu, chonde.” Pamenepo Yehova anamuyankha kuti: “Abweradi kuno.”+
11 Kodi anthu a mumzinda wa Keila adzandipereka m’manja mwake? Kodi Sauli abweradi kuno monga mmene ine mtumiki wanu ndamvera? Yehova Mulungu wa Isiraeli, ndiuzeni ine mtumiki wanu, chonde.” Pamenepo Yehova anamuyankha kuti: “Abweradi kuno.”+