Salimo 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anaweramitsa kumwamba n’kutsika.+Mdima wandiweyani unali kunsi kwa mapazi ake. Yesaya 64:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Zikanakhalatu bwino mukanang’amba kumwamba, mukanatsika pansi pano,+ komanso mapiri akanagwedezeka chifukwa cha inu,+
64 Zikanakhalatu bwino mukanang’amba kumwamba, mukanatsika pansi pano,+ komanso mapiri akanagwedezeka chifukwa cha inu,+