Deuteronomo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova Mulungu wanu adzabweza kwawo anthu a mtundu wanu amene anagwidwa ndi kupita kudziko lina,+ ndipo adzakumverani chifundo+ n’kukusonkhanitsaninso pamodzi kuchokera pakati pa anthu onse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.+ Ezekieli 36:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Ndidzakutengani pakati pa anthu a mitundu ina n’kukusonkhanitsani pamodzi kuchokera m’mayiko onse. Kenako ndidzakubweretsani m’dziko lanu.+ Ezekieli 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Uwauzenso kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga ana a Isiraeli kuchokera pakati pa mitundu ina ya anthu kumene anapita. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera m’mayiko owazungulira ndipo ndidzawabweretsa m’dziko lawo.+
3 Yehova Mulungu wanu adzabweza kwawo anthu a mtundu wanu amene anagwidwa ndi kupita kudziko lina,+ ndipo adzakumverani chifundo+ n’kukusonkhanitsaninso pamodzi kuchokera pakati pa anthu onse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.+
24 ‘Ndidzakutengani pakati pa anthu a mitundu ina n’kukusonkhanitsani pamodzi kuchokera m’mayiko onse. Kenako ndidzakubweretsani m’dziko lanu.+
21 “Uwauzenso kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga ana a Isiraeli kuchokera pakati pa mitundu ina ya anthu kumene anapita. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera m’mayiko owazungulira ndipo ndidzawabweretsa m’dziko lawo.+