Yobu 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+ Yobu 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndinkaphwanya nsagwada za wochita zoipa,+Ndipo wogwidwa, ndinkamulanditsa kukamwa kwa wochita zoipayo.
10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+
17 Ndinkaphwanya nsagwada za wochita zoipa,+Ndipo wogwidwa, ndinkamulanditsa kukamwa kwa wochita zoipayo.