Salimo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyang’aneni. Ndiyankheni, inu Yehova Mulungu wanga.Walitsani maso anga+ kuti ndisagone mu imfa.+ Salimo 61:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzatalikitsa moyo wa mfumu.+Zaka zake zidzachuluka kufanana ndi mibadwo yambirimbiri.+
3 Ndiyang’aneni. Ndiyankheni, inu Yehova Mulungu wanga.Walitsani maso anga+ kuti ndisagone mu imfa.+ Salimo 61:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzatalikitsa moyo wa mfumu.+Zaka zake zidzachuluka kufanana ndi mibadwo yambirimbiri.+