-
Yohane 19:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Choncho iwo anayamba kukambirana kuti: “Malaya awa tisawang’ambe, koma tiyeni tichite maere kuti tidziwe amene angatenge malaya amenewa.” Izi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, limene linati: “Iwo anagawana malaya anga akunja pakati pawo, ndipo anachita maere pa malaya anga amkati.”+ Chotero asilikaliwo anachitadi zimenezi.
-