Salimo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chake oipa adzatsutsidwa pa chiweruzo,+Ndipo ochimwa sadzapezeka pagulu la olungama.+ 1 Akorinto 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 kuti pasapezeke munthu wodzitama+ pamaso pa Mulungu.