Yobu 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Kodi ukudziwa nthawi yoikidwiratu imene mbuzi za m’mapiri zokhala m’matanthwe zimabereka?+Kodi unaona nthawi imene mphoyo zimabereka+ ndi zowawa za pobereka?
39 “Kodi ukudziwa nthawi yoikidwiratu imene mbuzi za m’mapiri zokhala m’matanthwe zimabereka?+Kodi unaona nthawi imene mphoyo zimabereka+ ndi zowawa za pobereka?