Genesis 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma ine ndidzabweretsa chigumula+ chamadzi padziko lapansi, kuti chiwononge chamoyo+ chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mphamvu ya moyo* m’thupi mwake. Chilichonse cha m’dziko lapansi chidzafa.+ Yobu 38:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndani anagawa ngalande ya madzi osefukira,Ndi njira ya mtambo wa mvula yamabingu,+
17 “Koma ine ndidzabweretsa chigumula+ chamadzi padziko lapansi, kuti chiwononge chamoyo+ chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mphamvu ya moyo* m’thupi mwake. Chilichonse cha m’dziko lapansi chidzafa.+