Salimo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova ndi Mfumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Mitundu yatheratu padziko lapansi.+ 1 Timoteyo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa Mfumu yamuyaya,+ imene siifa,+ yosaoneka,+ yekhayo amene ali Mulungu,+ kwa iyeyo kupite ulemu ndi ulemerero mpaka muyaya.+ Ame.
17 Kwa Mfumu yamuyaya,+ imene siifa,+ yosaoneka,+ yekhayo amene ali Mulungu,+ kwa iyeyo kupite ulemu ndi ulemerero mpaka muyaya.+ Ame.