Yobu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye waika abale anga enieni kutali ndi ine,+Ndipo ngakhale anthu ondidziwa andisiya. Salimo 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+
11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+