Luka 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yabwino yophera Yesu,+ pakuti anali kuopa anthu.+ Luka 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo khamu lonselo linanyamuka, onse pamodzi, n’kupita naye kwa Pilato.+
2 Komanso ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yabwino yophera Yesu,+ pakuti anali kuopa anthu.+