Miyambo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsoka limatsatira ochimwa,+ koma olungama ndi amene amalandira mphoto zabwino.+ Aroma 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense wochita zoipa, kuyambira Myuda+ mpaka Mgiriki,+ adzaona nsautso ndi zowawa.