Miyambo 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wolungama ndi amene amapulumutsidwa ku zowawa,+ ndipo woipa amalowa m’malo mwake.+ Yesaya 43:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chakuti ndiwe wamtengo wapatali kwa ine,+ ndimakulemekeza ndipo ndimakukonda.+ Ndidzapereka anthu m’malo mwa iwe, ndipo ndidzapereka mitundu ya anthu m’malo mwa moyo wako.+
4 Chifukwa chakuti ndiwe wamtengo wapatali kwa ine,+ ndimakulemekeza ndipo ndimakukonda.+ Ndidzapereka anthu m’malo mwa iwe, ndipo ndidzapereka mitundu ya anthu m’malo mwa moyo wako.+